You can’t grow crops without phosphorus

To grow properly, plants need water, light and air. They also need nutrients from the soil, including nitrogen, potassium, and phosphorus. All of these are important – but phosphorus especially, because it affects the plant early in its life. The plant needs it to build its root system, which is the basis for taking up other nutrients. Without enough phosphorus, plants are stunted and yield little.

Read more >>

Market waste can be an important source of compost  

 

Alimi ku Malawi akonzekera mvula

Malawi farmers prepared for the rains.

Ndi nyengo ya mvula yomwe ili pafupi alimi mdziko lonse la Malawi asosa kale minda yawo kuyembekezera kudzala mbeu. Demeter seed company yapereka kale mbeu mmasitolo osiyanasiyana oposela 900 mdziko lonse la Malawi kuti mlimi ayipeze mosavutikira ndi mdera lomwe akukhala.

Ndi sosa komanso mbeu zomwe zafika kale mmadera osiyanasiyana chiyembekezo cholandira mvula yabwino chilipo

With the rainy season approaching farmers throughout Malawi have prepared their lands for planting. The Demeter Seed company has made available seeds through over 900 outlets nationwide serving the farmer close to his home.

With lands prepared and inputs in place the rains can come and hopefully plentiful.

IMG-20181115-WA0014.jpg

 

 

 

Mbeu yomwe ingakwaniriyse zosowa za mlimi

Seeds to meet the needs of Malawi farmers

Demeter Agriculture ikupezeka ndi mbeu za chimanga zopilila ku chilala, zobereka kwambiri, zikonoka, zopilila ku namkafumbwe ndiponso zozuna dowe. Demeter Agriculture ikupezekanso ndi mbeu za mgulu la nyemba monga chuma, soya ndi Mtedza wa CG7.

Demeter Agriculture has the range of maize varieties which are drought tolerant, high yielding, poundable, long lasting to weavils and sweet when roasted. Demeter Agriculture has also legume such as chuma beans, soya and CG7 groundnuts

Kasinthasintha wa ulimi wa Mtedza ndi chimanga umabweretsa zokolora zochuluka

Groundnut planting with maize for better yields

Mukadzala mosinthanasinthana mbeu ya Mtedza ndi chimanga zimathandizila kukolola zochuluka pa mbeu zonse ziwirizi. Mtedza umagwiritsa ntchito chonde chotsalila mmunda mmene munali chimanga ndiponso umakozanso nthaka yomwe imapindulira chimanga / Groundnuts planted in rotation with maize improve the productivity of both crops. Groundnuts make good use of leftover nutrients while improving soil conditions for following maize crop.

Demeter seed yagawa kale mbeu ya Mtedza wa CG7  ndiponso ikupititiza kutero mmasitolo onse a Farmers World,  Agora ndi ma agrodealers osiyanasiyanasiyana mmadera onse omwe mumalimidwa Mtedza muno MMalawi / Demeter Seed is distributing seed of the groundnut variety CG7 to branches of Farmers World and AGORA as well as various agro-dealers in groundnut producing areas in Malawi.

Click here for more information on groundnut production.

 

 

6 things agroecology can do for farming and the environment

Agroecology has returned to the global spotlight, as one approach to bring farmers closer to meeting challenges [like rising food demand]. Agroecology emerged as a science which supports food security and sustainable agriculture. In the 1960s, it was studied as the interaction between crops and the environment …. Promoting farming systems that are beneficial to producers and society, as well as the earth’s ecosystems has become a central theme ….

Read more >>

 

Blog at WordPress.com.

Up ↑